With work almost completed, the Malawi-Mozambique Power interconnector project is set to be operational by September this year. This was revealed during a tour of...
Chipatala cha Queen Elizabeth (QECH) munzinda wa Blantyre chati tsopano makina ake atatu mwa asanu othandiza anthu amene ali ndi vuto la impsyo ayamba kugwira...
Apolisi munzinda wa Lilongwe amanga a Tsisa Mbangali azaka 26, powaganizira kuti anagwililira mlamu wawo wazaka 13 ndi kumupha. Ofalitsankhani za polisi ya Lilongwe, a...
Unduna wa zantchito, watseka mbali ina ya Makandi Tea Estate imene ili m’boma la Thyolo chifukwa chophwanya ena mwa malamulo antchito. Mbaliyi ndi kumene kuli...
Apolisi ya Nathenje m’boma la Lilongwe amanga a Luwashi Bakali, 26, powaganizira kuti apha mwana omupeza wazaka ziwiri. Izi zachitika m’mudzi wa Kawale kwa mfumu...
Ophunzira pa sukulu yaukachenjede ya University of Malawi(Unima) ku Zomba akhazikitsa chipangizo chothandiza anthu omwe ali ndi ulumali wosaona. Mmodzi mwa ophunzirawo, Hudson Mwangalika, wati...
Chileka Police Station has urged learners at Lipunga Primary School in Blanytre to work hard so that they become reliable future citizens. Led by Superintendent...
South West Police Region has commended the business community in the region for supporting them in strengthening security ahead of the festive season. Commissioner of...
Anthu a midzi ya Mphampha ndi Tsambalabooka kwa mfumu yaikulu Lundu ku Chikwawa ati ndi okondwa kuti tsopano adzimwa madzi aukhondo. Anthuwa anena izi kampani...