Bungwe la Civil Society Elections Integrity Forum ladzudzula mmodzi mwa atsogoleri a chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Norman Chisale kaamba ka mchitidwe olankhula mau...
Anthu okhala m’mudzi mwa a Gulupu a Kaname mdera la Mfumu yayikulu Chilikumwendo m’boma la Dedza ati apindula ndi ntchito yolumikiza magetsi m’madera akumudzi ya...
Boma la United Kingdom, kudzera ku bungwe la Global Health Partnerships, lakhazikitsa ntchito yothandizo kutukula luso la anthu ogwira ntchito zaumoyo m’dziko muno. Mlembi wamkulu...
Ena mwa atsogoleri amipingo m’dziko muno ati mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera waonetsa kusakondera kwake posankha anthu atsopano m’ma board a kampani za...
Wachiwiri kwa nduna yaza ulimi Benedicto Chambo anacheza ndi akuluakulu achipembezo chachi Rasta munzinda wa Lilongwe. A Chambo, omwenso ndi phungu wadera la Mangochi –...
Mtsogoleri wa zokambirana mu nyumba ya malamulo, a Richard Chimwendo Banda, wayamika mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera chifukwa chokhala ndi chikhulupiliro mwa amayi...
Akatswiri pa nkhani zamalamulo a Justin Dzonzi ndi a Allan Ntata ati ntchito ikadalipo kwa amene akutsogolera chipani cha UTM, a Dalitso Kabambe, pa nkhani...
Bungwe la Greenbelt Initiative Authority lapereka ntchito ya gawo lachiwiri lomanga malo a mthilira a Nthola-Ilola m’boma la Karonga kwa amene agwire ntchitoyi, a Kabiki...
Bungwe la Transporters Association of Malawi lati kukonza msewu wa Mangochi-Makanjira kudzathandizanso kwambiri kulimbikitsa ntchito za mtengatenga ndi malonda pakati pa dziko lino ndi la...
Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), yemwenso ndi nduna ya maboma ang’ono, umodzi ndi chikhalidwe, a Richard Chimwendo Banda, ndiye wanena izi ndikulimbikitsa...