Category : Nkhani
Adzudzula zipani zomwe zikufuna kuti MEC isagwiritse chiphaso cha unzika pazisankho
Gulu lina la a Malawi omwe akudzitchula kuti Mzika Zokhudzidwa ladzudzula mchitidwe wa zipani zina zandale zimene zikufuna kukakamiza bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC)...
NEEF yati sikupereka ndalama za ulere
Bungwe lobwereketsa ndalama la National Economic Empowerment Fund Limited (NEEF) lati sizoona kuti lasayina mgwirizano ndi mtsogoleri wa dziko lino kuti lidzipereka ku banja lililonse...
Anthu 87 a zipani zosiyanasiyana alowa MCP ku Mangochi
Anthu osachepera 80 ochokera zipani za DPP, UDF ndi zina alowa chipani cholamula cha Malawi Congres (MCP) ku Mangochi. Powalandira anthuwa, yemwe ali wachiwiri kwa...
Favoured Martha wathandiza ana asukulu ovutika 23
Oyimba nyimbo za uzimu, Favoured Martha, wapereka thandizo la yunifomu kwa ana 23 ovutika apa sukulu ya pulaimale ya Chilobwe ku Blantyre. Katswiriyu analimbikitsanso oyimba...
Amugwira akuba ma mita a Water Board
Apolisi ku Zomba amanga Patrick Mbiri wazaka 26 pomuganizira kuti waba mamita a madzi a bungwe la Water Board komanso zotsegulira madzi. Mneneri wapolisi ku...
Alimi aku Lilongwe asonkhanitsa K1.7 biliyoni yochitira ulimi
Nduna yoona zaulimi, a Sam Kawale lero ili nawo pamwambo umene wakonzedwa ndi alimi aku Lilongwe, amene asonkhanitsa ndalama zoposa K1.7 biliyoni zogulira zipangizo zaulimi....

