One of the celebrated tech entrepreneurs in South Africa and beyond, Mandla Lamba, has been nominated for the prest...
Read full articleThe Malawi Broadcasting Corporation (MBC) would like to invite applications from suitably qualified persons to fill...
Read full articlePresident Dr Chakwera says the signing of the Nacala Development Corridor Agreement, the Railway Agreem...
Read full articlePresident Dr Lazarus Chakwera says the launch of the Mozambique- Malawi Regional Interconnection project will help ...
Read full articleThe Ministry of Water and Sanitation has dissolved the National Water Resources Authority (NWRA) Board with i...
Read full articleLilongwe based Civil Society Organisations in collaboration with the Association of Environmental Journalists...
Read full articleAmuna ena kwa Nkalo m’boma la Chiradzulu aatidzimulana kwambiri m’modzi mwa iwo atadzudzula mzake kuti wamupininga kuti njerwa zake zomwe anatentha zisapsye bwino. Nkhaniyi ikuti amunawo ndipa chinzawo ndipo onse...
Mai wina ku Chilinde mu mzinda wa Lilongwe amuthamangitsa pa lendi chifukwa chosintha amuna ngati Malaya. Malinga ndi mtolankhani wathu kumeneko, maiyo yemwe ndi wosakwatiwa koma amagwira ntchito pa kampani...
Mwambo wodalitsa ukwati walepheleka pa tchalichi china ku Chigumula mu mzinda wa Blantyre zitadziwika kuti mkwati ali kale pa banja ndi mkazi wina. Nkhaniyi ikuti mwamunayo amakhala ndi banja lake...
Mayi wina ku Nguludi Turn-off, amuvumbulutsa pathengo, akuchita zadama ndi mlonda wina. Nkhaniyi ikuti mayiyo tsiku ndi tsiku, amatsanzika mwamuna wake chakumbandakucha kuti akupita ku madzi ndipo pozindikira vuto lamadzi...
Mkulu wina kwa Mfumu Masula mboma la Lilongwe amudula mlomo atamupezelera ndi mkazi wa mwini m’nyumba. Nkhaniyi ikuti mkuluyo ali ndi udindo waukulu m’mudzimo koma m’malo moti adzionetsa chitsanzo chabwino,...
Mnyamata wina m’dera la Mfumu Mabilabo mboma la Mzimba wabwelera lokumbakumba, atakomoka ndi kachasu. Nkhaniyi ikuti mnyamatayo ndi mbiya ng’ambe moti sizimatheka kukhala osamwa tsiku liri lonse. Nthawi zambii...
M’dera la Mfumu Wimbe mboma la Kasungu, mkulu wina yemwe anasiya mkazi wake kuno kumudzi kupita ku joni kukazisaka, wakhumudwa kwambili atamva kuti mkazi wakeyo ali ndi pathupi. Nkhaniyi...
Mkulu wina kwa Wimbe mboma la Kasungu wazunguzia mutu munthu wina yemwe sakudziwika atagwira njoka yake yokawa. Nkhaniyi ikuti mkuluyo ndi nkhalakale pa bizinesi koma zimamveka kuti ali ndi njoka...
Mkulu wina ku Thondwe mboma la Zomba wapita ku Lilongwe asakufuna, mbili itamveka kuti wapereketsa ndalama yokwana 200 thousand kwacha chifukwa chofuna kulemera. Nkhaniyi ikuti mkuluyo amachita geni kuyambira kalekale...
Anthu a m’mudzi wina mdera la Mfumu Mabulabo mboma la Mzimba anafa ndi phwete pamene mkulu wina anamenyedwa ndi mwana wachichepere chifukwa chozemba kubweza ngongole. Nkhaniyi ikuti m’deralo muli...
One of the celebrated tech entrepreneurs in South Africa and beyond, Mandla Lamba, has been nominated for the prestigious Global Emergi...
Read full articleA South African based electric vehicle manufacturer and green tech company, Agilitee Africa, has announced the launch of the world's fi...
Read full articleSuper League giants Nyasa Big Bullets have offloaded eight players after the expiry of their respective deals, the club says in a state...
Read full articleThe Malawi national football team, the Flames will be part of the 16 teams that will battle it out for a place in the last eight of the...
Read full articleIn an apparent act of open defiance, some top Democratic Progressive Party (DPP) officials continue to use the picture of the party&rsq...
Read full articleThe Malawi Broadcasting Corporation has issued an invitation to International Competitive Bidding for Outside Broadcasting Van as elabo...
Read full articleThe UK Government has removed all eleven African countries off England’s red list, easing travel restrictions. ...
Read full article