Category : Nkhani
Amayi a Zokonda Amayi apulumuka pangozi
Gulu la amayi a Zokonda Amayi a m’chigawo chakummwera lapulumuka pa ngozi ya bus imene yachitika m’boma la Ntcheu usiku wa Lachitatu. Amayiwa amachokera munzinda...
MANEPO yayamikira Madam Chakwera polimbana ndi nkhanza za anthu achikulire
Mkulu wa bungwe la MANEPO, a Andrew Kavala, wayamikira mayi wa dziko lino, Madam Monica Chakwera, pa chidwi chawo choonetsetsa kuti achikulire m’dziko muno asamazunzidwe....
Madam Chakwera ayamikira Press Trust potukula maphunziro
Mayi wa pfuko lino, Madam Monica Chakwera, athokoza bungwe la Press Trust pochirimika pa ntchito zotukula maphunziro m’dziko muno. Madam Chakwera anena izi ku Chiyola...
Madam Chakwera atsegula sukulu ya Chiyola CDSS
Mayi wa pfuko lino, Madam Monica Chakwera, atsegulira sukulu yatsopano ya sekondale yoyendera ya mdera la Chiyola m’boma Rumphi imene bungwe la Press Trust lamanga....
Tisewera kuti tibwezeretse ulemu wathu – Mabedi
Mphunzitsi wa timu yaikulu ya mpira wa miyendo m’dziko muno, Patrick Mabedi, wati waauza anyamata ake kuti mawa adzasewere ndicholinga chofuna kubwezeretsa ulemu kudziko lino...
Senegal yachita zokonzekera pa Bingu Stadium
Timu ya Senegal yachita zokonzekera zake lero pa Bingu National Stadium, pamene ikuyembekezeka kukumana ndi timu ya Malawi mawa. Mphunzitsi wa timuyi ongogwirizira, Pape Thiaw,...
Zokonzekera zamwambo wa MBC Zokonda Amayi zili mchimake
Wapampando wamwambo wa MBC Zokonda Amayi wa chaka chino, mayi Mervis Senga, ati zonse zokonzekera zamwambo wa Zokonda Amayi Macheza umene uchitikire munzinda wa Mzuzu...
Dr Usi amema ogwira ntchito m’boma kuti atsatire malonjezo a maiko olemera ku COP29
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wati ndi udindo wa akuluakulu a boma, kuphatikizapo aku unduna oona zachilengedwe ndi kusintha kwa nyengo,...
Illovo itolera ndalama zolimbikitsa ukhondo wa atsikana msukulu
Kampani yopanga sugar ya Illovo yakonza ntchito zosiyanasiyana zofuna kutolera ndalama zothandizira ukhondo wa atsikana msukulu zina zamdziko muno. Izi zikuchitika pansi pantchito ya Rise...

