Anthu awiri afa ku Thyolo potsatira zipolowe zomwe zinadza kutsatira mikangano ya ufumu wa Mankhamba pakati pa mayi Elizabeth Paulo komanso Laison Folopezi. Zipolowezi zinayambika...
Bungwe la International Monetary Fund (IMF) lati lipitiriza kuthandiza dziko lino kuti chuma chake chipitilire kupita patsogolo. Mkulu owona zofalitsa uthenga ku IMF, a Julie...
Boma la Neno likuchita bwino pa ntchito yolimbana ndi kachirombo koyambitsa matenda a edzi, kudzera mu ndondomeko yotchedwa HIV/AIDS Intergrated Initiative, bungwe la National Aids...
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yati ikufuna kuti bungwe la Football Association of Malawi lilowerere pazomwe zinachitika pamasewero awo ndi timu ya MAFCO lamulungu...
Bungwe loyang’anira masewero ampira muligi yaikulu ya mdziko muno la Super League of Malawi (SULOM) ladzudzula mchitidwe omwe timu ya Mafco yachita omwe ndi otsutsana...
Katswiri ochita zisudzo m’dziko muno Jamil Chikakuda ndipo amatchuka ndi dzina loti Che Mandota wati mphoto ya MBC Entertainers of Year ndiyo ya phindu kuposa...
Nduna yoona zaulimi a Sam Kawale yati anthu oposa 1.4 million ndi omwe ali mu kaundula olandira zipangizo zaulimi zotsika mtengo pa ndondomeko yaboma ya...
Kampani ya Serato Media Group, imene yakhala ikuthandiza kugulitsa nyimbo za Zeze Kingston, yathetsa m’gwirizano ndi oyimbayu patatha zaka zinayi akugwira ntchito limodzi. Kalata yochokera...
Mlembi wa mkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Richard Chimwendo Banda, wachenjeza aMalawi kuti asamvere atsogoleri andale amene adayeserapo koma adakanika kutukula dziko...