Gule kuwonetsa luso lophwanya njerwa pa ndende ya Maula mumzinda wa Lilongwe. Chindime ndi Phunkwaku komanso magulu oimba, ndi gule wamkulu wa pa ndendeyi ndi...
Prezidenti wa chipani Cha PP, Dr Joyce Banda walengeza kuti chipanichi chidzakhala ndi msonkhano wake waukulu pa 7 September chaka chino mumzinda wa Lilongwe. Iwo...
Kuli khwimbi la undipondera mwana pa bwalo la Nancholi mu mzinda wa Blantyre pamene mtsogoleri wakale wa dziko llino Dr Joyce Banda akuchititsa msonkhano. A...
Mwambo oyika m’manda malemu Moses Dossi, omwe anaakhalapo olembankhani za masewero komanso nduna ya zamasewero mu ulamulo wa boma la chipani cha United Democratic Front,...
Mwambo opereka malo kwa atsikana osewera mpira wa miyendo mutimu ya Scorchers wayamba ndi kupereka zikalata zaumwini kwa osewerawa ku unduna wa zamalo ku Lilongwe,...
A Saudi Fund for Development ati afulumizitsa ntchito yojambula msewu wa Makanjira ku Mangochi kuti ntchito yomanga msewuwu iyambe mwachangu. Izi akuti zikutengera chidwi chomwe...