Bungwe la Malawi Agriculture and Industrial Investment Corporation (MAIIC) lapanga phindu lokwana K2.5 billion chaka chatha poyerekeza ndi K722 million mu chaka cha 2022, malinga...
Yemwe anaakhalapo mkulu wa nthambi ya CID, a George Mnjale, amwalira lero ku chipatala cha Kamuzu Central mumzinda wa Lilongwe kumene amalandira thandizo. A Mnjale...
Dziko la Malawi latsegula ofesi ya ukazembe m’dziko la Israel kaamba kofuna kuti dziko lino lipindule ndi ntchito za ulimi ndi mtengatenga, mwa zina. A...
Chipatala cha Zomba Mental chati chili ndi anthu 27 amene anamaliza kulandira thandizo la mankhwala koma amakanika kuti atuluke chifukwa abale awo amawakana. A Harry...
Alimi a fodya m’dziko muno ati ndiosangalala ndi m’mene malonda a fodya ayambira pa msika. President wa Tobacco Association of Malawi (TAMA) trust, a Abiel...
Bwalo lalikulu ku Lilongwe laimitsa kaye mlandu wokhudza mmwenye ndi mavenda aku Nsungwi ku Area 25. Mavenda omwe amagulitsa zinthu za hardware ku msika wa...
Apolisi ku Chikwawa amanga nzika ziwiri za dziko la China poziganizira kuti zamenya ndikukomola Silaj Maluwa wazaka 37 pomuganizira kuti anaba mafuta a galimoto. Wachiwiri...
Bungwe la Malawi Union of Savings and Credit Cooperatives (MUSCCO) lapempha alimi m’dziko muno kuti asagulitse mbewu zawo kwa ochita malonda osatsata ndondomeko ndi cholinga...