Category : Nkhani
Mlandu authetsa, mavenda akufuna chipepeso
Bwalo la Milandu la High Court mumzinda wa Lilongwe lathetseratu mlandu wa pakati pa ochita malonda a ku Nsungwi, Area 25 ndi m’mwenye Akbar Salahudding...
Anthu apitilira kukhuza maliro a bambo Kapusa
Nduna yoona za madzi komanso ukhondo, mayi Abida Mia, pamodzi ndi anthu ena ambiri, asonkhana ku Machinjiri Area 3 mu mzinda wa Blantyre kumene akukhuza...
Ulimi wa nkhuku ndiothandiza
Mawanja oposa makumi awiri ku Choma mu mzinda wa Mzuzu ati ali ndi chiyembekezo kuti ulimi wa nkhuku omwe bungwe la SOS lawathandiza uli ndikuthekera...
Mavenda aku Nsungwi asonkhana ku High Court
Anthu ochita malonda ochokela ku Nsungwi ku Area 25 mu mzinda wa Lilongwe asonkhana panja pa bwalo la High Court kumene akuyembekezera kuti amve chigamulo...
Bushiri apereka chimanga kwa mabanja 200 ku Mangochi
Mneneri Shepherd Bushiri wagawa matumba a chimanga kwa mabanja okwana 200 amene anakhudzidwa ndi vuto lakusefukira kwa madzi m’dera la Mfumu yayikulu Nankumba ku Monkey-Bay...
Nditha kusiyira sukulu panjira — Mphatso
Mnyamata wina, Mphatso Sidiki, wadandaula kuti atha osalemba nawo mayeso aboma a Form 4 ngati sipapezeka ena omuthandiza kulipira nyumba yokhalamo komanso school fees, zonse...
Chitetezo munthawi ya chisankho ndi chofunika
Msonkhano wa akuluakulu a m’maboma mchigawo chakumpoto uli mkati komwe nkhani yaikulu ndi ya chitetezo panthawi ya chisankho, chomwe chichitike chaka chamawa. Poyankhula pamene amatsekulira...
‘Kalembetseni chiphaso cha unzika kuti mudzavote’
Msungichuma wa chipani cha MCP, a Albert Mbawala, alimbikitsa anthu mdera la Lilongwe Kumachenga kuti akalembetse chiphaso cha unzika pomwe kalembera wayamba m’boma la Lilongwe,...
Tikambe zabwino za dziko lathu — JB
Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Dr Joyce Banda, wapempha a Malawi kuti adzikamba zinthu zabwino zokhudza dziko lino kuti lipite patsogolo. Dr Banda, omwe ndi...

