A Kondwani Nyasulu awasankha kukhala mfumu ya mnzinda wa Mzuzu pazisankho zomwe zikuchitika mu mzindawu zosankha mfumuyi komanso wachiwiri wake. A Nyasulu, amene ndi a...
Bungwe la Greenbelt Authority lagulitsa matumba a chimanga okwana 3,300 ku nkhokwe za bungwe la National Food Reserves Agency (NFRA). Mkulu wa Greenbelt Authority, a...
M’modzi mwa akatswiri oyimba nyimbo za Hip-hop komanso katakwe paza Graphic Designing, Kennedy Mwenya, yemwe amatchuka kuti Spiral, wamwalira pangozi ya galimoto ku Mzuzu. Malipoti...
Alimi a ziweto a m’boma la Chikhwawa adandaula kaamba kakusagwira ntchito kwa malo osambitsako ziweto (dip), zomwe ati zikupereka chiopsyezo cha chigodola. Izi zadziwika pamene...
Khonsolo ya mnzinda wa Lilongwe yati siinamange malo okwelera bus aliwonse atsopano munzindawu ndipo malo aku Area 46 ku Grand Business Park ndi ongoyembekezera. Mkulu...
Inkosi ya Makosi Mbelwa V yatsogolera mafumu m’boma la Mzimba kukapepesa President Dr Lazarus Chakwera pa imfa ya amene anali wachiwiri wawo Dr Saulos Chilima...
Adindo a khonsolo ya Mbelwa ati ntchito yomanga bwalo la masewero la Mzimba ikhala ikufika kumapeto pofika m’mwezi wa December chaka chino. M’modzi mwa akulu...
Bungwe la Chiwalo Youth Network lalangiza achinyamata a m’boma la Phalombe kuti athandize kulimbikitsa ukhondo m’makomo mwawo komanso m’malo a boma monga ku Polisi ndi...