Category : Nkhani
K15 Million ndiyomwe ikufunika kuthandizira Peter Mlangeni
Oyimba nyimbo zauzimu amene akonza mwambo wamaimbidwe ndi cholinga chothandiza nzawo Peter Uyu Mlangeni, yemwe adavulala pangozi yagalimoto, ati pakufunika K15 Million kuti Mlangeni alandire...
Adakali mu ululu
M’modzi mwa oyimba nyimbo zauzimu m’dziko muno, Peter Uyu Mlangeni, adakali mu ululu kutsatira ngozi ya galimoto chaka chatha m’mwezi wa September. M’modzi mwa anzake...
Ogonana okhaokha chigamulo mawa
Bwalo lalikulu la milandu loona zamalamulo ku Blantyre likuyembekezeka kupereka chigamulo chake mawa ngati kuli koyenera kuti anthu ochita mchitidwe ogonanana amuna kapena akazi okhaokha...
Bus ya Bullets inakalibe mmanja mwa khothi
Bus ya FCB Nyasa Big Bullets sinabwerere kuma ofesi atimuyi, dzulo italandidwa ndi ma Sherrif. Bus-yi inalandidwa kaamba koti timuyi inali ndi ngongole ya ndalama...
Onesimus achenjeza akonzi a Ku Mingoli Bash
Phwando la nyimbo la Ku Mingoli Bash likuyenera kupitilira opanda Onesimus potsatira pempho la oyimbayu kuti achotsedwe pamndandawu kaamba koti akonzi aphwandoli sanatsate dongosolo. Akuluakulu...
Wapha munthu chifukwa cha nsanje
Apolisi ku Mulanje akufunafuna Joseph Louis yemwe akumuganizira kuti wapha Brian Mwaliwa wazaka 30. Louis anapha Mwaliwa atamupeza akuchita zadama ndi mkazi wake. Zadamazi amachitira...
Greenbelt Authority aiyamikira
Bungwe la National Food Reserve Agency (NFRA) komanso unduna wa zaulimi ayamikira bungwe la Greenbelt Authority kaamba ka matumba oposa 3000 a chimanga omwe awagulitsa...
M’busa wapereka mimba kwa mtsikana atamunamiza kuti amuchiritsa matenda
Apolisi ku Mulanje amanga m’busa wina, Steven Zambia, wazaka 38, pomuganizira kuti wakhala akugwililira mtsikana wazaka 15 kuchokera mwezi wa February mpaka June chaka chino...
Olembankhani ndi mlatho wazochitika ku nyumba ya malamulo — CSAT
Bungwe la Centre for Social Accountability & Transparency (CSAT) lati ndi koyenera kuti olembankhani azidziwa komanso kutsatira bwino momwe nyumba ya malamulo (Parliament) imagwilira ntchito...

