Bungwe la Chiwalo Youth Network lalangiza achinyamata a m’boma la Phalombe kuti athandize kulimbikitsa ukhondo m’makomo mwawo komanso m’malo a boma monga ku Polisi ndi...
Ana pafupifupi 1, 200 asiyira sukulu pa njira munzinda wa Lilongwe pakati pa miyezi ya April ndi June chaka chino chokha chifukwa cha umphawi komanso...
Katswiri oyimba nyimbo za Amapiano, Temwa, wati iye ndi odzipereka kuthandiza ana osowa amene agonekedwa mu zipatala m’dziko muno. Temwa amayankhula izi pa chipatala cha...
Wachiwiri watsopano kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wati adzipereka kwathunthu kuthandiza Prezidenti Dr Lazarus Chakwera potukula dziko lino komanso kukweza aMalawi. Iwo...
Anthu ena alipanja pa nyumba ya malamulo pomwe ayika kanema pofuna kupereka mwayi kwa anthuwo oonelera mwambo wolumbilitsa Dr Michael Bizwick Usi kukhala wachiwiri kwa...
Mkulu wa timu ya Silver Strikers Patrick Chimimba wati chidwi chikhale pa zomwe Bullets yachita povomereza ndikupepesa ku timu ya Silver osati ndalama zomwe apereka....
Timu ya Silver Strikers yati K6 million imene FCB Nyasa Big Bullets yapereka ndi yosakwanira kukonzetsera bus yawo imene idaphwanyidwa pa ziwawa zomwe zidachitika ku...
Wapampando watsopano wa bungwe loyendetsa zisankho la MEC, Justice Annabel Mtalimanja, alumbilitsidwa lachisanu pa 21 June, 2024 ku Lilongwe High court nthawi ya 9 koloko...
Katswiri pa utsogoleri ndi ufulu wa anthu, a Undule Mwakasungula, ati kusankhidwa kwa Justice Annabel Mtalimanja ngati wapampando wa bungwe la MEC ndi chilimbikitso kwa...
Bungwe la Admarc tsopano lidzigula chimanga pa mtengo wa K700 pa kilogramme (K35,000 pa thumba la 50 kilogrammes), malinga ndi mkulu wa bungweli, a Daniel...