Bungwe la Malawi Network of People Living with HIV and AIDS (MANET+) lapereka njinga yamoto ku ofesi ya zaumoyo ya Mzimba North yomwe ithandizire pantchito
Nduna ya zofalitsa nkhani yomwenso ndi mneneri wa boma, a Moses Kunkuyu akuchititsa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe pa lipoti la ngozi ya ndege yomwe
Ofesi yoona zofalitsa nkhani mu ofesi ya mlembi wamkulu wa boma ndi nduna OPC yalangiza atolankhani kuti apitirize kugwira bwino ntchito ndi boma. Mneneri wa
Akuluakulu a mpingo wa CCAP mu synod ya Livingstonia akukumana ku Embangweni ku tchalichi cha Laudon m’boma la Mzimba. Moderator wa Mpingowu M’busa Rueben Msowoya
Mpingo wa Manja Seventh Day Adventist mu nzinda wa Blantyre lero ukumalizitsa msonkhano wake wa pachaka wa Misasa omwe unayamba pa 27 August 2024. Mutu
Mwambo wa chionetsero cha ntchito zokopa alendo komanso chikhalidwe wayamba ndi ulendo wa ndawala kuchokera pa Memorial Tower mpakana mu msewu wa Presidential Drive munzinda
Renowned Engineer Vitumbiko Mumba is now the manager of Amidu Ellan Muonjeza, famed for the song ‘Udikerebe’. Mumba, who previously managed the late Wambali Mkandawire,
Bwalo la milandu la First Grade m’boma la Mzimba lalamula a Emmanuel Khowaya,32, kuti akagwire ukayidi wa kalavula gaga kwa zaka khumi ndi ziwiri atawapeza
Katswiri oyimba Dancehall, Malinga Mafia, wapepesa kwa okonda nyimbo zake kaamba kokanika kuyimba ku phwando lamayimbidwe la Illusionz lomwe likuchitikira pagombe m’boma la Mangochi. Katswiriyu