Category : Nkhani
Oyimbira mpira wamiyendo awapempha kuti agwire ntchito mwaukadaulo
Chinthuzi : Football Association of Malawi Anthu wokonda masewero a mpira wamiyendo m’dziko muno atsindika zakufunika koti oyimbira masewerowa agwire ntchito yawo mwaukadaulo pofuna kuti...
Muli ndi ufulu olowa chipani chomwe mwafuna – Brown Mpinganjira
Mmodzi mwa akuluakulu a chipani cha Malawi Congress Party (MCP) m’chigawo chakum’mwera, a Brown Mpinganjira, apempha anthu a m’boma la Thyolo kuti asamaope kapena kuopsezedwa...
Amumanga ataba mbendera yadziko
Apolisi ku Mulanje amanga Shadreck Medson wazaka 22 pomuganizira kuti waba mbendera zadziko zokwana zisanu ndi imodzi – 6 kwa Nkhonya m’boma la Mulanje. Ofalitsankhani...
Tilime mbewu zambiri zopilira ku n’gamba — Bushiri
M’neneri Shepherd Bushiri wa mema aMalawi kuti ayambe kulima mbewu zosiyanasiyana komanso zimene zili zopilira ku ng’amba ndi cholinga chofuna kupewa njala. A Bushiri amayankhula...
Anthu oposa 600 atuluka DPP ndikulowa MCP ku Mulanje
Anthu omwe anali mamembala a chipani cha DPP okwana 619 ochokera m’madera a kummwera komanso pakati m’boma la Mulanje, alengeza kuti atuluka chipanichi ndipo alowa...
Anthu ena akusowabe pokhala – Paramount Chief Kaduya
Mfumu yaikulu ya Alhomwe, Paramount Chief Kaduya, yapempha boma ndi anthu akufuna kwabwino kuti athandizebe pomangira nyumba anthu 1161 amene akusowabe pokhala kutsatira namondwe wa...
Asanu agwidwa ataba zipangizo zomangira bwalo la timu ya Wanderers
Apolisi ku Soche mu mzinda wa Blantyre amanga alonda awiri a kampani ya zomangamanga ya AFECC komanso anthu atatu ochita malonda pa sitolo ya hardware...
Atsogoleri a zipembedzo alimbikitsa umodzi pa chikumbutso
Atsogoleri azipembedzo zosiyanasiyana alimbikitsa umodzi pakati pa aMalawi, pomwe patha chaka chimodzi dziko lino litakumana ndi namondwe wa Freddy. Ena mwa alalikiwa ndi Phophet Shepherd...

