Khwimbi la anthu likukhamukira ku bwalo la zamasewero la Mulanje kumene kukhale mwambo wokumbukira kuti patha chaka chimodzi chichitikireni Namondwe wa Freddy. Prezidenti wa dziko...
Bungwe la ophunzira pa sukulu ya ukachenjede ya MUBAS la Students Representative Council lati likhala likulangiza ophunzira pasukuluyi pa kagwiritsidwe ntchito kabwino kandalama zomwe amapatsidwa...
Unduna owona za chilengedwe ndi kusintha kwa nyengo wati ndiokhumudwa ndimomwe anthu akupitilizira kuononga nkhalango m’dziko muno. Mmodzi wa akuluakulu ku undunawu, a Titus Zulu,...
Ophunzira pa sukulu ya ukachenjede ya Mubas, yomwe kale inkaziwika kuti Polytechnic, athokoza mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera pokweza ndalama zomwe ophunzirawa amalandira...
Boma lati ligula mankhwala ochuluka obaya othandiza kuchepetsa kufala kwa kachilombo ka HIV kumapeto achaka cha 2025 ndicholinga chothadiza pantchito yolimbana ndikufala kwa kachilomboka. Mkulu...
Prezidenti wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, watsimikizira anthu a m’boma la Dowa kuti vuto la madzi likhala mbiri ya makedzana. Poyankhula kwa khwimbi la...
Banki ya National yapanga phindu lokwana K71.96 billion, boma litadulapo kale msonkho mu chaka cha 2023. Phinduli lakwera poyerekeza ndi phindu la K45.9 billion limene...
Ophunzira akale apasukulu ya sekondale ya Bwaila, kudzera mu gulu limene adakhazikitsa la Bwaila Social Welfare, loweruka anakapereka katundu osiyanasiyana kwa anthu ovutika komanso amene...