Malawi Broadcasting Corporation
Agriculture Development Local Local News Nkhani

Tilime mbewu zambiri zopilira ku n’gamba — Bushiri

M’neneri Shepherd Bushiri wa mema aMalawi kuti ayambe kulima mbewu zosiyanasiyana komanso zimene zili zopilira ku ng’amba ndi cholinga chofuna kupewa njala.

A Bushiri amayankhula izi ku Masasa mu mzinda wa Mzuzu komwe iwo amagawa chimanga kwa anthu amene njala idawakhudza.

“Monga ine kumunda kwanga ndinalima chinangwa chambiri ndipo chachita bwino kwambiri,” iwo anafotokoza.

A Bushiri ali ndi chikonzero chofuna kufikira maanja okwana 1 Million ndipo ati padakali pano anthu okwana pafupi-fupi 600,000 ndi amene athandizidwa kale.

Olemba: Henry Haukeya
#MBCOnlineServices

Print Friendly, PDF & Email

Related posts

Tecno Mobile helps flood-hit families in Nkhotakota

Alinafe Mlamba

COURT TO RULE ON SATTAR’S ACCOUNTS

MBC Online

Malawi Judiciary launches e-courts

Olive Phiri
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.