Malawi Broadcasting Corporation
Nkhani

Anthu oposa 600 atuluka DPP ndikulowa MCP ku Mulanje

Anthu omwe anali mamembala a chipani cha DPP okwana 619 ochokera m’madera a kummwera komanso pakati m’boma la Mulanje, alengeza kuti atuluka chipanichi ndipo alowa Malawi Congress (MCP).

Mmodzi wa akuluakulu a MCP, a Brown Mpinganjira, Wapampando wa chipanichi ku Mulanje komanso wachiwiri kwa mkulu wa achinyamata mchipani cha MCP, a Blessings Chilembwe, ndiwo alandira anthuwa pamwambo umene unachitika pa Mulanje paboma.

Related posts

Bangwe yapha Bullets

MBC Online

Dedza Dynamos yatola chikwama

MBC Online

‘Musalole andale kukutumani kuti muchite ziwawa’

Romeo Umali
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.