Category : Nkhani
Young Stunna wafafaniza machimo ku Blantyre
Anthu amunzinda wa Blantyre anali okondwa kwambiri ataonelera maimbidwe ochititsa chidwi kuchoka kwa oimba wa chamba cha amapiano, Young Stunna, wochokera m’dziko la South Africa....
Atsogoleri azipembedzo alimbikitsa bata
Bungwe la atsogoleri azipembedzo zosiyanasiyana m’dziko muno la Religious Leaders Organisation lapempha anthu kuti adzikhala mwabata nthawi zonse ndi kulemekeza atsogoleri adziko. Mtsogoleri wabungweli, Sheikh...
Munthu mmodzi wavulala modetsa nkhawa pa ngozi ya sitima
Munthu mmodzi wavulala modetsa nkhawa pa ngozi ya sitima ku Blantyre mu njanji ya Magalasi – Nyambadwe – kudutsa ku Chapima. Ofalitsankhani za polisi ya...
Anthu akondwa kuona sitima ikulunjika mtunda wa Mchinji
Anthu ambiri ku Area 25 ku Lilongwe ndi madera ozungulira m’mawa wa lero Loweluka anasonkhana pa mlatho wa Area 49 pa msewu wopita ku Nsungwi...

