Bungwe la Chewa Heritage Foundation (CHEFO) lati chaka chino mwambo wa Kulamba ukhalapo ku Mkaika m’boma la Katete mdziko la Zambia. Yemwe akulumikizitsa mafumu pankhani...
Boma lati ndilokhumudwa ndi momwe ntchito yomanga msewu ochokera ku Chitipa kupita ku Ilomba ikuchedwera kufika kumapeto. Nduna yoona za mtengatenga, a Jacob Hara, ndiwo...
Anthu okhala m’mudzi mwa Kanyenda, dera la mfumu Kabudula chakumpoto kwa boma la Lilongwe tsopano ali ndi madzi aukhondo kutsatira mjigo omwe bungwe la National...
Mafumu apempha boma ndi mabungwe kuti athandize malo osamalira ana amasiye a Zoe Foundation komanso Temwani Chilenga, mtsikana amene akusamalira ana amasiye okwana 92 m’dera...
Ana atatu mwa 100 alionse ndi okwinimbira m’dziko muno, kafukufuku amene achita pa sukulu ya ukachenjede ya LUANAR watsimikizira izi. M’modzi mwa akuluakulu pa sukuluyi,...
Oyimba nyimbo za uzimu ati ndi okondwa ndi momwe nzika za mu nzinda wa Lilongwe zinabwelera pa phwando la maimbidwe limene linachitikira ku Sheaffer lolemba...