Mwini wake wa kampani imene imagulitsa zipangizo zophodera za amayi ya the Nail Room, Atupele Chindevu, wati adzithandiza ligi ya chigawo chapakati yampira wamanja popereka...
Olemba: Timothy Kateta Zokonzekera za mwambo wa misa yapadera yokumbukira yemwe adali wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, malemu Dr Saulos Chilima, zili mkati ku Nsipe...
Khonsolo ya mu mzinda wa Zomba yati ndiwokondwa kuti boma la Dr. Lazarus Chakwera tsopano laikapo chidwi pomalizitsa ntchito zachitukuko zomwe zinayamba zaima kaye kaamba...
Mphunzitsi watimu ya FCB Nyasa Big Bullets Kalisto Pasuwa wati ali ndichikhulupiliro kuti timu yake iyambaso kuchita bwino mu Super League masana ano pamene akukumana...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi wapempha anthu ogwira ntchito m’boma kuti adzigwira ntchito modzipereka pofuna kutukula dziko lino, mogwirizana ndi masomphenya...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Dr Micheal Usi, alonjeza kuti apitiriza masomphenya achitukuko a malemu Dr Saulosi Chilima. Iwo ati agwirizana kale ndi Prezidenti Dr...
Oyankhulapo pa nkhani za ndale a Undule Mwakasungula ati kuchoka kwa a Dalitso Kabambe ku chipani Democratic Progressive (DPP) kutha kukhala kukhumudwa chifukwa a Peter...
Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati pakufunika m’gwirizano wa mphamvu pakati pa bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) ndi mabungwe amene amagwira nawo...
Ophunzira ena amene akulemba mayeso a Form Four ku Mangochi achedwa kulemba mayeso awo mmawa walero kaamba kakuti mapepala a mayeso amene amafuna kulemba sanafike....
Komiti yoona za matenda a Covid 19 siyidayankhulepo kanthu pambuyo pa malipoti osonyeza kuti munthu m’modzi wapezeka ndi nthendayi m’boma la Mangochi. Malinga ndi mmodzi...