Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi ati ndi okhumudwa kuti ena mwa aphungu anyumba ya malamulo sakuonetsa chidwi chogwiritsa ntchito ndalama zonse...
Dr Micheal Usi, amene ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, ati achita zotheka polimbikitsa chipani cha UTM, monga mtsogoleri wachipanichi, kuti chikhale champhamvu. Iwo...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi atsimikizira anthu aku Mulanje kuti alandira ngongole zoti achitire bizinesi ndicholinga chotukula miyoyo yawo. Wachiwiri kwa...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera, wati atsogoleri amipingo ali ndi ntchito yaikulu yothandiza kupititsa patsogolo ntchito zachitukuko m’dziko muno. Dr Chakwera alankhula izi...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, lero akhala nawo pa mwambo wa mapemphero pa mpingo wa Monkey Bay Assemblies of God m’boma la Mangochi....
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera m’mawa uno ali pa ulendo oyendera ntchito zachitukuko m’boma la Mangochi. Dr Chakwera akuyembekezeka kuyendera komanso kucheza ndi...