Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wati aMalawi akuyenera kugwira ntchito molimbikira kuti dziko lino lipeze chuma. Dr Chakwera ati zina mwa ntchito zimene...
President Dr Lazarus Chakwera and President of Mozambique, Dr Filipe Jacinto Nyusi, are expected to open this year’s Agriculture Fair at Chichiri Trade Fair Grounds...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi akuchita nawo mapemphero pa mpingo wa Zambezi Evangelical ku Mitsidi mu mzinda wa Blantyre. Pampingopa palinso...
Unofficial results for the local government by-election conducted by the Malawi Electoral Commission (MEC) in Chilaweni Ward, Blantyre Rural East Constituency show that independent candidate...
Dr Micheal Usi, amene ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, ati achita zotheka polimbikitsa chipani cha UTM, monga mtsogoleri wachipanichi, kuti chikhale champhamvu. Iwo...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi atsimikizira anthu aku Mulanje kuti alandira ngongole zoti achitire bizinesi ndicholinga chotukula miyoyo yawo. Wachiwiri kwa...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi wapempha anthu ogwira ntchito m’boma kuti adzigwira ntchito modzipereka pofuna kutukula dziko lino, mogwirizana ndi masomphenya...
Expectations are high that the construction of Masukambiya Health Post at Group Village Headman Masukambiya in Chikwawa Mkombezi will improve health service delivery in the...
Jean Sendeza, the Minister of Gender, Community Development and Social Welfare says the accountability programme for the elderly, known as AFFORD, has played a vital...