Prezidenti Dr Lazarus Chakwera wati zokambirana zimene anali nazo ndi mafumu aku Machinga zayenda bwino. Dr Chakwera watsimikizira anthu a m’bomali kuti ali ndi chidwi...
Ntchito yoponya voti pachisankho chapadera chosankha khansala wa dera la Mwasa ili mkati m’boma la Mangochi. Pamene imakwana 5:30 m’mawa, anthu ochuluka anayamba kufika pamalo...
Ena mwa anthu amene amagwiritsa ntchito misewu ya mu mnzinda wa Lilongwe ati ndi okondwa ndi mmene ntchito yomanga misewu mu mnzindawu ikuyendera. Poyankhula ndi...
Bungwe lotolera misonkho la Malawi Revenue Authority (MRA) lalangiza anthu amene ali ndi galimoto zawo pachipata cha Songwe Border Post kuti akaombole galimotozi ati chifukwa...
Unduna wa za umoyo wati ndi okhudzidwa ndi kuchuluka kwa matenda amu ubongo m’dziko muno zitadziwika kuti anthu 281 ndi amene adzipha kuyambira mwezi wa...