Sukulu ya ukachenjede ya Emmanuel imene ndi ya mu mnzinda wa Lilongwe yalengeza zoyamba kuphunzitsa Kiswahili ngati phunziro lapadera. Izi zadziwika pa mwambo okondwelera chilankhulochi...
Maiko a Malawi ndi Tanzania akuchita nawo mwambo okondwerera tsiku la chiyankhulo cha Kiswahili munzinda wa Lilongwe. Mwambowu umachitika pofuna kulimbikitsa umodzi pakati pamaiko komanso...
Bungwe la Clean Cities Project pamodzi ndi khonsolo ya mzinda wa Lilongwe m’mawa uno likuyenda ulendo wa ndawala umene akutola zinyalala ndi kulimbikitsa anthu kuti...
Nthambi yoona za anthu ochoka mmaiko ena kukagwira ntchito ku Israel yatsimikizira anthu komanso boma la Malawi kuti aMalawi okagwira ntchito kumeneko adzikalandira ndalama zosachepera...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera, masana ano akuyembekezeka kucheza ndi ochita malonda ochokera mmisika yosiyanasiyana ya kuchigawo chakummawa kwa dziko lino. Ochita malonda...
Msonkhano wa bishop a maiko a Malawi, Zambia komanso Zimbabwe watha m’boma la Salima pomwe agwirizana zogwilira limodzi komanso kutumikira mokomera nkhosa zao maikowo pa...
Anthu oposa 146,000 a m’maboma a Ntcheu ndi Balaka akuyembekezeka kukhala ndi madzi abwino komanso aukhondo kudzera ku ntchito yopopa madzi mu nthaka pogwiritsa ntchito ...