Category : Nkhani
President Chakwera awonekera m’nyumba ya malamulo
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, lero akawonekera ku nyumba ya malamulo ndikukayankha mafunso kuchokera kwa aphungu anyumbayi. Potsimikiza izi, mneneri wa Boma, a...
A Chakwera asankha a Mazalale ngati mlembi wa mapulani achitukuko
Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus Chakwera wasankha a Jacob Mazalale ngati mlembi mu unduna wa zachuma oona za mapulani achitukuko. A Mazalale, amene ndi...
“Palibe atafe ndi njala” — Kunkuyu
Nduna ya zofalitsa nkhani yemwenso ndi m’neneri wa boma, a Moses Kunkuyu, ati mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera watsindika kuti palibe munthu amene...
Nzika za China zikakhala mndende zaka zisanu ndi chimodzi
Bwalo la Magistrate mumzinda wa Lilongwe lagamula kuti nzika zitatu zadziko la China zikakhale mndende kwa zaka zisanu ndi chimodzi atazipeza olakwa pa mlandu ozembetsa...
Tipitiriza kuthandiza – NBS Bank
Bank ya NBS yathandiza anthu okalamba komanso a ulumali ndi matumba a ufa wa chimanga kummwera kwa boma la Chiradzulu. Poyankhula popereka thandizoli, mkulu wa...
Mankhwala oletsedwa mmasewero atha kuononga mbiri ya dziko – MADO
Bungwe lomwe limawona za mchitidwe ogwiritsa ntchito mankhwala osaloledwa mmasewero la Malawi Anti-Doping Organisation (MADO) lati kugwiritsa ntchito mankhwala oletsedwa mmasewero kuli ndikuthekera koipitsa mbiri...
A Malawi Mudzifunsa Mafunso Atsogoleri Anu Mmalo Momangodandaula — Usi
Nduna yoona za chilengedwe ndi kusintha kwa nyengo, Dr Michael Usi, yalangiza a Malawi kuti adzitha kumafunsa mafunso atsogoleri awo mmalo momangodandaula akaona kuti zinthu...
MNENERI BUSHIRI WAGAWA CHIMANGA KU THYOLO
Prophet Shepherd Bushiri wagawa chimanga kwa Nchilamwera m’boma la Thyolo komwe wapempha anthu kuti asalowetse ndale pa thandizo lake. Mneneri Bushiri wati apitirizabe kupereka chimanga...
PROPHET SHEPHERD BUSHIRI AGAWA CHIMANGA M’MABOMA AKUM’MWERA KUMAPETO ASABATAYI
Ntchito yogawa chimanga chaulere kwa anthu ovutika yomwe akuchita mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering the Jesus Nation Prophet Shepherd Bushiri ipitilira nchigawo chakummwera...

