Phungu wanyumba ya malamulo wa dera la kumpoto chakummawa kwa boma la Machinga, Ajilu Kalitendere, walangiza anthu a m’dera lake kuti alandire ufa umene boma...
Apolisi ku Lingadzi mu mzinda wa Lilongwe apeza zipangizo za wailesi ya Radio Maria zimene mbava zinaba masiku apitawa za ndalama yoposa K90 million. Malinga...
President Lazarus Chakwera wati khalidwe lonyoza anthu achikulire powanena kuti ndi mfiti ndi kuwapha (mob justice) zili ndi kuthekera kosokoneza ana achichepere m’dziko muno. A...
Yemwe anali wachiwiri kwa prezidenti wachipani cha Democratic Progressive Party (DPP), a Uladi Mussa, wati agwira ntchito limodzi ndi atsogoleli achipani cha MCP pofuna kuonetsetsa...
Wogwira ntchito ku bungwe la ADMARC Malani Kaira wazaka 35 ndi amzake awiri: Isaac Bisayi wazaka 39 ndi Imran Mtonda wazaka 30, awamanga powaganizira kuti...
Mtsogoleri wa dziko, Dr Lazarus Chakwera, wayamikira sipika wanyumba ya malamulo, a Catherine Gotani Hara, kamba kaluntha lake potsogolera nyumbayi. Polankhula pomwe akuwonekera mnyumbayi, Dr...
Bwalo la Magistrate ku Lilongwe lili mkati momva mlandu wa a Norman Chisale yemwe anali wachitetezo wa mtsogoleri opuma wa dziko lino, Professor Arthur Peter...