Category : Nkhani
SHUGA ADZIPEZEKA OKWANIRA – ILLOVO
Kampani yopanga ndikugulitsa shuga ya Illovo yati anthu asade nkhawa ndikusowa kwa shuga komwe kwakhalapo pakatipa,ponena kuti vutoli litha. Akuluakulu a kamaniyi anena izi mu...
TEVETA ILIMBIKITSA ACHINYAMATA OMWE ADASIYIRA SUKULU PA NJIRA KULIMBIKIRA NTCHITO ZALUSO
Mkulu wa bungwe lophunzitsa ntchito za luso la manja la Technical Entrepreneur and Vocational Education and Training Authoritiy (TEVETA), a Elwin Sichiola, alimbikitsa achinyamata amene...
APOLISI KU LIMBE ALONJEZA KUPEREKA CHITETEZO CHOKWANIRA
Mkulu watsopano wa Polisi ya Limbe, a Edwin Mkhambo, watsimikizira anthu ochita malonda mderali komanso madera ozungulira kuti aonetsetsa kuti kuli chitetezo chokwanira. A Mkhambo...
KAMPANI ZACHITA BWINO CHAKA CHATHA— MCCCI
Kafukufuku yemwe bungwe la amalonda la Malawi Confederation of Chambers of Commerce and Industry (MCCCI) lachita waonetsa kuti kampani 50 mwa 100 zilizonse m’dziko muno...
SILVER STRIKERS YASAYINA OSEWERA WACHITATU TSOPANO
Timu ya Silver Strikers yasayina amene anali osewera kutsogolo kwa timu ya Dedza Dynamos, Charles Chipala, pa mgwirizano wa zaka zitatu. Chipala wasewereraponso matimu monga...
MPUNGWEPUNGWE KUNYUMBA YAMALAMULO
Kuli mpungwepungwe ku nyumba ya malamulo pomwe zokambirana kunyumbayi zayamba ndipo a Kondwani Nankhumwa komanso a Mary Navicha anaimilira ngati mtsogoleri wa zipani zotsutsa. Awiriwa...
CHITUKUKO CHIFIKIRE MADERA ONSE — ZIKHALE
Mmodzi wa akulu akulu mchipani cha MCP yemwenso ndi nduna yaza Chitetezo Chadziko a Ken Zikhale Ng’oma ati boma lipitiriza kutukula madera onse a dziko...
MAFUMU ATENGE MBALI POTHETSA NJALA M’DZIKO MUNO
Nduna ya maboma ang’ono a Richard Chimwemdo Banda yalangiza mafumu kuti adzionetsetsa kuti pali chilungamo pothandiza anthu a m’midzi. A Chimwendo Banda omwenso ndi...

