Dr Chakwera ayendera chitukuko cha mphepete mwa nyanja ku Mangochi
Mtsogoleri wadziko lino, Dr Lazarus Chakwera, lero akuyendera ntchito zosiyanasiyana zachitukuko m’boma la Mangochi. Kuchoka apo, Dr Chakwera ayendera ntchito yomanga ofesi yatsopano ku khonsolo

