Apolisi ku Bunda m’boma la Lilongwe agwira anthu awiri powaganizira kuti adapha mlamu wawo, a Luciano Masiye a zaka 26, pomumenya ndikukwilira thupi lake ku...
Bungwe la Malawi Bureau Standards (MBS) lati kugwira ntchito limodzi ndi nthambi zina zaboma nkofunika pa ntchito zolimbikitsa chilungamo pa malonda, mwazina. Mkulu wa bungweli,...
Aphungu a nyumba ya malamulo a kukambirana ganizo lokhazikitsa lamulo lomwe livomereze ulimi wa chamba chakwathu kuno. Phungu wa dera la kumwera kwa boma la...
Akatswiri pa nkhani za malonda a zachuma ati akukhulupilira kuti kutsegulira kwa msika wa fodya mwezi wamawa kutha kuthandizira kuti ndalama yakwacha ikhazikike. Iwo anena...
Pamene anthu ena akupitilira kusautsika ndi vuto la njala m’boma la Mangochi, Mneneri Shepherd Bushiri wapeleka chimanga kwa anthu amene amakhala pafupi ndi Goshen city...
Ochita malonda a zovala zakaunjika mu mnzinda wa Lilongwe akuchita zionetsero kamba kakukwera kwa misonkho pa mabelo a zovalazi. Pakali pano, ochita malondawa afika pa...
Mneneri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG), Shepherd Bushiri, wadzudzula mchitidwe olanga ana mopitilira muyeso akalakwitsa, ponena kuti izi ndi nkhanza. Iwo anena izi...