Mmodzi mwa akuluakulu a chipani cha MCP ku nyumba ya malamulo, a Ulemu Chilapondwa, adzudzula aphungu anyumba ya malamulo kamba ka khalidwe losapereka ulemu kwa...
Mlingo wa kukwera mtengo kwa zinthu (inflation rate) watsika mu February chaka chino kufika pa 33.5 percent kuchoka pa 35 percent mu January. Izi ndi...
Apolisi ku Lilongwe agwira a Anthony Chimpale a zaka 48 omwe amagwira ntchito kunthambi ya Land Resource and Conservation ku unduna waza malimidwe. Malinga ndi...
Anthu oposa 18,000 okhala mumzinda wa Lilongwe alandira chimanga chaulere lamulungu kuchokera kwa mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering the Jesus Nation, Prophet Shepherd...
Ena mwa anthu 2000 opindula Mtsogoleri wa Mpingo wa Salvation for All Ministries International, Apostle Clifford Kawinga, wati ulimi wa mthilira ungathandize dziko lino kukhala...
Khoti lina m’boma la Phalombe lalamula a Paul Mwina a zaka 35 zakubadwa kuti akagwire jele kwa zaka 14 chifukwa adagwililira mwana omupeza wazaka 12...
Khothi la Magistrate ku Blantyre lalamula amuna awiri ndi mayi m’modzi kuti apereke chindapusa pa milandu yosiyanasiyana yomwe anapalamula. Anthuwa ndi a Chifundo Kauwa, 38,...
Apolisi ku Chileka mu mzinda wa Blantyre amanga anthu anayi atapezeka ndi ndalama zachinyengo zokwana K915,000. M’neneri wa polisi ya Chileka, a Jonathan Phillipo, wati...
A khonsolo yamzinda wa Lilongwe, mogwirizana ndi asilikali achitetezo, agumula ndikusalaza sitolo zimene zinaamangidwa mphepete mwa manda ku dera la Nsungwi ku Area 25 ku...