Anthu omwe akukhala ku misasa ya Nyamvuwu, Matiki ndi Ngala ku Nkhotakota kaamba ka madzi osefukira m’nyanja ya Malawi ati akusowa zinthu zambiri zofunika pa...
Yemwe anali mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma ku nyumba ya malamulo, Kondwani Nankhumwa, walengeza kuti watula pansi udindowu. Iwo ati zikhala zovuta kupitilirabe kukhala pa...
Mtsogoleri wa chipani chatsopano cha People’s Development (PDP), Kondwani Nankhumwa, wati chipanichi chabwera kudzasintha Malawi kukhala dziko lodzidalira pa chakudya, la umodzi ndinso kulimbikira pantchito....
Bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo m’dziko muno la FAM lati likupanga chothekera kuti lidzikhala mu ubale wabwino ndi kampani komanso anthu ochita za...
A Jacob Hara, omwe ndi nduna ya za mtengamtenga, apempha anthu m’dziko muno kuti akhale odekha pamene boma likuyesetsa kukonzanso misewu. Ndunayi yayakhula izi pomwe...
Timu ya Dedza Dynamos tsopano izidziwika kuti Premeir Bet Dedza Dynamos kutsatira m’gwirizano umene yakhazikitsa ndi kampani ya Premier Bet wa ndalama zokwana K100 million...