Nduna yoona za chilengedwe, a Michael Usi, yauza akuluakulu osiyanasiyana ogwira ntchito za kafukufuku zokhudza nsomba kuti agwiritse ukadaulo wawo ndi kuonetsetsa kuti achitapo kanthu...
Bungwe lolimbikitsa kuti amayi adzikhala m’maudindo akuluakulu la NGO Gender Cordination Network lati ladandaula kuti a Mary Navicha, omwe anali mtsogoleri wa aphungu a chipani...
M’modzi mwa akatswiri wotola zithunzi m’dziko muno, Ras Peter Kansengwa, wati tsopano akupeza bwino ku chipatala komwe ali cha Artemis m’dziko la India. Poyankhula ndi...
Wapampando wa kampani ya Ekhaya Farm’s Foods, Thom Mpinganjira wapereka K17 million kwa osewera mpira akale omwe anachita zakupsa mzaka za 1978 ndi 1979 komanso...
Ndalama zokwana K80.4 million ndi zomwe zapezeka pa masewero amu ligi ya TNM apakati pa matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru Wanderers...
Mkhalakale pa ndale yemwenso ndi m’modzi wa akuluakulu a chipani cholamula cha Malawi Congress (MCP) a Brown Mpinganjira apereka uthenga wachiyembekezo kwa anthu akudera la...
Phungu wadera la Chikwawa Nkombezi, a Abida Mia yati aMalawi ayembekezere ntchito zachitukuko zochuluka pansi pa utsogoleri wa Dr. Lazarus Chakwera. Phunguyi yemwenso ndi nduna...
Katswiri watsopano womwetsa zigoli wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers yemwe kwawo ndi ku Cameroon, Sama Thierry Tajong, ndi wokayikitsa ngati asewere nawo Blantyre Derby...