Category : Nkhani
WORLEC calls for equality, inclusivity for women in politics
Women’s Legal Resources Centre (WOLREC) has stressed the need to uphold principles of equality and inclusivity in the political arena. Maggie Banda, WOLREC’s Executive Director,...
Tabitha ndi katswiri mbambande ku France
Katswiri wampira wamiyendo wa asungwana wadziko lino, Tabitha Chawinga,amene akusewerera timu ya PSG ku France, amusankha kukhala osewera amene wakankha chikopa mododometsa mu ligi yakumeneko...
Boma lipitiriza kufikitsa zitukuko mmadera onse — Chimwendo Banda
Mkulu wa achinyamata m’chipani cha Malawi Congress (MCP) yemwenso ndi nduna ya maboma ang’ono, a Richard Chimwendo Banda, walangiza anthu amdera lakuzambwe m’boma la Mangochi...
Mussa Ajibu asambitsa chokweza Vissah
Mnyamata wadzigogodo wamdziko muno,Mussa Ajibu, lero wagonjetsa mnyamata wamtali ochokera m’dziko la South Africa, Ruan Vissah pamasewero ankhonya amene anachitikira munzinda wa Lilongwe. Majaji onse...
Blue Eagles yayamba moyo wa ligi ya Chipiku ndichipambano
Timu ya Blue Eagles, yomwe idatuluka mu ligi yaikulu chaka chatha, yayamba ulendo wake wa ligi ya m’chigawo chapakati ya Chipiku ndi chimwemwe pomwe yathambitsa...
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yagumula sitolo zoposa 60 mkatikati mwa Lilongwe
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe m’mbandakucha walero wagwetsa ndi kugumula nyumba zoposa 60 zogulitsira katundu ntauni ya munzinda wa Lilongwe kamba koti eni ake anazimanga...
Akhazikitsa chipani chatsopano
Malipoti akusonyeza kuti mtsogoleri wambali ya aphungu otsutsa boma kunyumba yamalamulo, a Kondwani Nankhumwa, akhazikitsa chipani chatsopano chotchedwa People’s Development Party (PDP). Malinga ndi kalata...

