Malawi Broadcasting Corporation
Local Nkhani

Tajong atha osasewera nawo Blantyre Derby

Katswiri watsopano womwetsa zigoli wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers yemwe kwawo ndi ku Cameroon, Sama Thierry Tajong, ndi wokayikitsa ngati asewere nawo Blantyre Derby kaamba koti sanalandilmrebe chilolezo chosewera mpira kapena kugwira ntchito mdziko muno (Work permit) pa chingerezi.

Kumayambiliro kwa sabata ino, Tanjong anasaina mgwirizano wa zaka ziwiri  ndi timu ya Wanderers.

Padakali pano timu-yi ikuyesetsa  kuti katswiri-yu apeze chilolezo chosewera masewero ake woyamba pomwe Wanderers ikukumana ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets masanawa mu ligi ya TNM.

 

Olemba Amin Mussa

Related posts

Mumba pledges volunteers’ labour policies reformation

Romeo Umali

Scorchers aim for a clean sheet, a win

Romeo Umali

Azaumoyo akufufuza za imfa ya achinyamata aku Manase

Rabson Kondowe
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.