Kampani yofulula mowa ya Castel, yakhazikitsa chakumwa chatsopano chimene akuchitcha kuti Pomme Breeze. M’modzi mwa akuluakulu a kampaniyi, a Fiona Nyambo, ati chakumwa chaukali chimenechi...
Apolisi ku Soche mumzinda wa Blantyre amanga amuna ena awiri, kuphatikiza pa atatu omwe anawagwira kale mwezi wa March, pa mlandu wakuba ndikuvulaza munthu ku...
Apolisi ku Mulanje akusunga m’chitokosi a Chikumbutso Sailesi a zaka 32 zakubadwa powaganizira kuti adapha mayi wina wazaka 65. Malinga ndi ofalitsankhani wa Polisi ya...
Anthu okhala kwa Jumbe ku Machinjiri ati sakumvetsa kuti anamanga malo awo ochitira malonda pamwamba pa paipi yaikulu yamadzi a Blantyre Water Board, katundu ochuluka...
Bungwe la Malawi Red Cross Society masana ano lapereka thandizo la ndalama kwa mabanja omwe anakhudzidwa ndi madzi osefukira m’boma la Nkhotakota pa msasa wa...
Nzika ya ku Niger, a Osman Muhammad, akuyisunga ku ndende ya Maula khoti litakana pempho lake la belo. Lachitatu masana, Muhammad anakaonekera kubwalo la Magistrate...
Apolisi agwira nzika yaku Niger pabwalo la ndege la KIA itabisa mankhwala woopsya kumalo wochitira chimbudzi. Apolisi apabwaloli ati Osman Mohamed, amene ndiwa zaka makumi...
Bungwe la mpingo wakatolika la Catholic Development Commission of Malawi (CADECOM) lapereka ndalama zokwana K63,150,000 ku mabanja 421 omwe akhudzidwa ndi njala kwa Mfumu yaikulu...