Apolisi ku Lilongwe amanga a Ruth Nkhoma powaganizira kuti anapha amuna awo a Misheck Bayison powakoka ndi kupotokola ziwalo zobisika kaamba kakusamvana pa ndalama yokwana...
Apolisi ku Lilongwe agwira anthu awiri omwe akuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi kubedwa kwa katundu wambiri mu mzindawu komanso kuchita ziwembu. M’neneri wa Polisi ya Kanengo,...
Bungwe la Malawi Council of Disability Affairs (MACODA) lapempha olembankhani m’dziko muno kuti adzilemba nkhani zomwe zingalimbikitse ufulu wa anthu omwe ali ndi ulumali. Mkulu...
Anthu asanu ndi atatu amene amakumba manda ku manda a Area 18, pansi pa Lilongwe City Council, alandira njinga komanso K250,000 aliyense ngati njira imodzi...
Mkulu wa bungwe lowulutsa mawu la Malawi Broadcasting Corporation (MBC), a George Kasakula, ati bungwe lawo lidzagwira ntchito mwaukadaulo ndi mopanda kukondera pa chisankho cha...
Anthu okhala mu nzinda wa Lilongwe omwe analembetsa mu ndondomeko ya Mtukula Pakhomo wam’mizinda akuyembekezeka kulandira ndalamazi lachinayi, zomwe ndi K150,000 aliyense. Anthu 22 339...
Thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, malemu Dr Saulos Chilima, aliyika m’manda pamudzi wa Mbirimtengelenji pa Nsipe m’dera la Senior Chief Inkosi Champiti m’boma...
Oyimira akubanja kwa mayi Mary Chilima, bambo Ziliro Chiwambo, anati akuyamika mtsogoleri wa dziko lino komanso aMalawi chifukwa cha chikondi chomwe aonetsa pa zovutazi. Iwo...