Katswiri oyimba amene amachokera m’boma la Phalombe, Giboh Pearson, wapulumuka pa ngozi ya galimoto yomwe wachita pomwe amapita ku phwando la msangulutso ku Bangwe mu...
Lingadzi Police Station is keeping in custody 26-year-old Lovemore Chikopa for allegedly defrauding business individuals of millions of Kwacha. Lingadzi Police’s publicist, Cassim Manda, says...
Thupi la yemwe anali muulutsi ku MBC, mayi Everess Kayanula, anyamuka nalo mawa kuchoka ku Blantyre kupita kumudzi kwawo kwa Msiro, mfumu yayikulu Kayembe m’boma...
Gulu lovina dansi pa pologalamu yapa wailesi ya Kale Langa imene imauluka pa MBC Radio one yasonkhana mu mzinda wa Mzuzu kumene akuvina dansiyo. Mkonzi...
President wa dziko lino watsindika kufunika koti anthu m’dziko muno akhale ogwirizana komanso mwa bata ndi mtendere ndikuyika zonse mmanja mwa Chauta, pambuyo pa chiphyinjo...
Chataika Makawa wazaka 45 ali mchitokosi cha polisi ku Mangochi pomuganizira kuti wapha mkazi wake Esimy Daudi wazaka 42, amene amamukayikira kuti anali ndi chibwenzi....
Khonsolo ya mnzinda wa Lilongwe usiku uno ikugwira ntchito yosesa komanso kuchotsa zinyalala mu munzindawu. Mfumu yamnzindawu, a Esther Sagawa, ndiyo ikutsogolera ntchitoyi yomwe yayambira...