Zokonzekera za mwambo wa mapemphero okumbukira ufulu wa dziko lino zili mchimake
Zokonzekera za mwambo wa mapemphero okumbukira kuti dziko lino latha zaka 60 likudzilamulira omwe uchitike loweruka pa 6 July zili mchimake. MBC inayendera malo omwe...

