Kuli chikondwelero ku Parish ya mpingo wa Katolika ya Nzama m’boma la Ntcheu pamene akukhazikitsa nyengo yokondwelera kuti papita zaka 125 chiyikhazikitsireni. Malinga ndi Bambo...
Popitiriza ndi ulendo wake m’chigawo chakummawa kwa dziko lino, Prezidenti Dr Lazarus Chakwera lero ayendera chitukuko chosiyanasiyana m’boma la Balaka. Mtsogoleri wadziko linoyu ayendera Demeter...
Oyimba wamkazi Puleng Phoofolo pamodzi ndi munthu wina amene amayendetsa galimoto ali m’chipatala cha Boitumelo m’dziko la South Africa kutsatira ngozi imene achita dzulo masana...
Ofesi yoona za chisamaliro cha anthu munzinda wa Lilongwe yati dziko la Malawi likhoza kudzakhala ndi m’badwo wa anthu amene sadzidzakwanitsa kupereka chisamaliro choyenera kwa...
Mkulu wa kampani ya Magic promotions, a Brazio Mathias, ati chilichonse chikuyenda bwino pamene akukonzekera kuti aonetse koyamba kwa aMalawi kanema wawo otchedwa “Justice” amene...
Mkulu wa kampani ya NACALA Logistics, a Chandra Mahon Singh, ati kuyambira sabata ya mawa adzikwanitsa kubweretsa malita a mafuta okwanira 2 million ndipo ati...
Wapampando wa bungwe loona za chisankho la Malawi Electoral Commission, Justice Annabel Mtalimanja, wati ndi okhutira ndi mmene chisankho chapadera chayendera m’maboma a Mangochi ndi...