President Dr Lazarus Chakwera wati boma likudziwa kuti m’dziko muno muli vuto losowa nyumba. Koma iye wati boma lake layambapo ntchito yotchedwa – Project 250....
Mlembi wamkulu wa chipani cha UTM a Patricia Kaliati wati malemu Dr Saulos Chilima anaonetsa chitsanzo chabwino potumikira dziko lino modzipereka posayang’ana zigawo. A Kaliati...
Mkulu wa Chimbota Community Development Organisation m’boma la Nkhatabay a Kevin Troughton wati posachedwapa bungweli limanga chipatala ku Bwelero mdera la Sub – TA Ndola...
Nduna ya za madzi ndi ukhondo yomwenso ndi phungu oimira dera la Chikwawa Mkombezi, Abida Mia, lero anayendera zitukuko zomwe akhazikitsa posachedwapa kuphatikizapo mijigo yokwana...
Phungu wadera la Kumachenga m’boma la Lilongwe a Ezra Ching’onga adandaula kuti ophunzira ambiri omwe amalemba mayeso a MSCE mdera lake sasankhidwa kupita ku university...
Yemwe anali mlendo olemekezeka pa mwambo owonetsa kanema wa Justice ku Lilongwe a Dalitso Kabambe wapempha a Malawi kuti aziikapo chidwi potukula aluso a mdziko...
Bwalo la milandu la Magistrate munzinda wa Lilongwe lati lipitiriza kumva mulandu wa oganiziridwa kuti amafalitsa nkhani zabodza kudzera pa intaneti a Chiyanjano Mbedza, Lachiwiri...
Bwalo la milandu la Magistrate munzinda wa Lilongwe likuyembekezeka kupereka chigamulo pa pempho la belo la a Chiyanjano Mbedza, amene akuwaganizira kuti amafalitsa nkhani zabodza...