Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wapempha aMalawi kuti atengepo gawo pa ntchito yokonzanso chuma cha dziko lino mu njira zosiyanasiyana monga kulimbika pa...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wamema anthu amene amayendetsa ntchito zosamalira anthu kuti asamakondere pa ntchito monga za mtukula pakhomo. Dr Chakwera anapemhanso...
Apolisi ku Limbe munzinda wa Blantyre akusunga mwana amene akuti makolo ake anamusiya pa golosale ina kwa Manje. Ofalitsankhani pa Polisi ya Limbe, a Aubrey...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wayatsa magetsi pa sitolo za Luviri m’boma la Mzimba muntchito yopereka magetsi akumudzi ya MAREP. Luviri ndi imodzi...
Masana ano bwalo la Magistrate mnzinda wa Lilongwe likuyembezeka kupereka chigamulo pa pempho labelo lomwe oyimira a Chiyanjano Mbedza anapereka sabata yatha. A Mbedza anawamanga...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati ndiokhutira ndi momwe ikuyendera ntchito yokonzanso msewu wa M1. Dr Chakwera anena zimenezi pa Mtengowanthenga pomwe analankhula...
Wapampando wa chipani cha Malawi Congress (MCP) m’chigawo chapakati a Zebron Chilondola ayamikira anthu a m’boma la Mangochi kaamba kowonetsa chikhulupiliro mu chipanichi. A Chilondola...
Khwimbi la anthu lasonkhana pa Mtengowanthenga m’boma la Dowa, pamene akudikila mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, kuti awalankhule pamene iye akudutsa pa ulendo...
Wapampando wa komiti ya Public Accounts a Mark Botomani ati ndi okhumudwa kaamba ka kuchedwa komaliza kwa ntchito yokonza msewu wa pa Kammwamba. Msewuwu ndi...