Phungu wa dera laku m’mwera kwa Msinja m’boma la Lilongwe, a Francis Belekanyama, wapempha achinyamata kuti asiye kudziyang’anira pansi pazochitika zokhudza ndale m’dziko muno. A...
Bishop Mthandizi Suzgo Nyirenda wa Diocese ya Mzuzu mu mpingo wa Katolika wapempha aMalawi kuti alilire Mulungu ndi cholinga choti dziko lino lilandire mayankho pa...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi akuchita nawo mapemphero pa mpingo wa Zambezi Evangelical ku Mitsidi mu mzinda wa Blantyre. Pampingopa palinso...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera pamodzi ndi mayi wa fuko lino Madam Monica Chakwera akuyembekezeka kukhala nawo pa mapemphero a misa pa mpingo...
Chikho cha mpira wa miyendo cha Tambala Super tsopano achikhazikitsa ndipo adzipikisana ndi matimu ang’onoang’ono a m’boma la Blantyre. Chikhochi ndi cha ndalama zokwana K10...
The launch of the K10 million Tambala Super Cup is currently underway at Kumanda Football Ground in Chileka, Blantyre. Sponsored by Amazon Group Limited, the...
Inkosi ya Makhosi M’mbelwa V yati aMalawi akuyenera kupewa m’chitidwe wa ziwawa chifukwa dziko lino limakonda mtendere. Inkosiyi imayankhula izi pa mwambo wa Umthetho ku...
AChewa pansi pa bungwe lawo la Chewa Heritage Foundation (CHEFO) atsekulira mudzi wa aChewa, m’mudzi wa Msampha, mfumu yaikulu Chadza m’boma la Lilongwe. Mudzi wa...
Phungu wa Nyumba ya Malamulo ku Chikwawa Nkombezi, Abida Mia, apereka thandizo la chakudya kwa mabanja okwana 3000 a m’dera lawo amene akhudzidwa ndi njala...