Chakwera ali pa mkumano ndi mabungwe othandiza pa ngozi zogwa mwadzidzidzi
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera akukumana ndi nthumwi za mabungwe akunja amene ndi okhudzidwa ndi ngozi zomwe zinagwa mwadzidzidzi m’dziko muno. Mkumanowu ukuchitikira...

