Ntchito yogula magetsi ku Mozambique yatsala pang’ono kuyamba
Adindo amene akumanga Matambo Substation m’dziko la Mozambique ati aMalawi ayembekezere kupitilira kukhala ndi magetsi odalilika pamene ntchito yogula magetsi m’dzikolo ikuyembekezeka kuyamba pofika mwezi...

