Mkulu watsopano wa achinyamata m’chipani cha Malawi Congress (MCP), a Steve Baba Malondera, wapempha achinyamata ku chigwa cha mtsinje wa Shire kuti akhale ndi chidwi...
Dziko la Malawi lasayinira mgwirizano ndi kampani zomwe zimapanga komanso kuyendetsa ntchito za sitima za pamadzi kuti zidzayambitse ntchitoyi pa nyanja ya Malawi. Mtsogoleri wa...
Boma lapempha anthu ochita ndale m’dziko muno kuti asamalowelere ntchito za ma khonsolo ndi cholinga chofuna ku kwaniritsa zolinga zawo pa ndale. Nduna ya za...
Mtsogoleri wa dziko la Malawi wayamikira boma la Mozambique kaamba ka ubale wabwino omwe ulipo panopa umene wachititsa kuti dzikolo lipereke malo ku Nacala oti...
Osewera masewero othamanga anayi amene ali ndi ulumali osaona akhala akupita m’dziko la France posachedwapa kuti akapikisane nawo ku mpikisano wa 2024 Paris Paralympic. Nduna...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera akuyembekezeka kukambirana ndi kampani zoona za sitima zapamadzi ku Germany kuti athandize kuyambitsa ntchito za maulendo pa nyanja...
Bungwe la Tobacco Commission lalangiza alimi a fodya m’dziko muno kuti ayambiretu ku konzekera ulimi wa fodya wa chaka cha mawa chifukwa kuzula mwachangu fodya...
Apolisi ku Mangochi amanga a Boika Sabiti, 48, atawapeza ndi chida choopsya chopangidwa ndi zitsulo zosongoka komanso zokuthwa. Ofalitsa Nkhani pa Polisi ya Mangochi, a...