Bwalo lamilandu ku Mangochi lalamula Boika Sabiti wazaka 48 kuti akakhale ku ndende zaka zisanu ndi chimodzi chifukwa chopezeka ndi chida choopsa chopangidwa ndi zitsulo...
Apolisi ku Lilongwe agwira a Chikumbutso Ngilazi amene amagwira ntchito ku chipatala cha Kamuzu Central powaganizira kuti akhala akuba mankhwala a nkhaninkhani. Malinga ndi ofalitsankhani...
Kampani ya ku Germany yopanga magetsi a dzuwa ya Sun Power Africa Development yasainira mgwirizano ndi boma la Malawi odzayambitsa ntchito yopanga magetsi okwana 50...
Ofalitsa nkhani ku chipani cha Malawi Congress (MCP), a Jessie Kabwila, ati chipani chotsutsa cha DPP chidanena bodza ku msonkhano wawo waukulu pamene adati m’dziko...
Bungwe la National Registration Bureau (NRB) lati linalemba anthu okwana pafupifupi 12.3 million chiyambireni ntchito yakalembera wa unzika m’chaka cha 2016. Mkulu wa ntchito ya...
Ofalitsa nkhani za boma, a Moses Kunkuyu, ati boma ndi lokhudzidwa kwambiri ndi imfa za anthu 26 omwe amwalira pangozi ya galimoto m’boma la Kasungu...
Mlembi Wamkulu watsopano wa chipani cha Malawi Congress(MCP), a Richard Chimwendo Banda, wati boma ladzipereka pokweza dera laku chigwa cha Shire komanso dziko lonse la...
Mkulu watsopano wa achinyamata m’chipani cha Malawi Congress (MCP), a Steve Baba Malondera, wapempha achinyamata ku chigwa cha mtsinje wa Shire kuti akhale ndi chidwi...