Anthu ambiri m’boma la Mangochi ndi maboma ena a m’chigawo cha kumvuma akondwera ndi kuyambanso kwa ntchito yopanga zitupa zoyendera zomwe ikuchita nthambi ya Immigration...
Bungwe la Pharmacy and Medicines Regulatory Authority (PMRA) latsutsa kafukufuku wa sukulu ya ukachenjede ya m’dziko la Ethiopia lomwe linati dziko la Malawi muli chiwerengero...
Anthu okhala m’boma la Mangochi ndi maboma ena ku chigawo cha kumvuma tsopano ali ndi kuthekera kopangitsa zitupa zoyendera nthambi ya Immigration italengeza kuti iyambiranso...
Bungwe loyendetsa zisankho m’dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) yalengeza zotsatira za chisankho cha komiti yaikulu ya chipani cha Democratic Progressive. A Joseph Mwanamvekha...
Akuluakulu a bungwe loona zachisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) ayamba ntchito yoonkhetsera ma voti omwe nthumwi ku msonkhano waukulu wachipani cha DPP...
Prezidenti Dr Lazarus Chakwera wafika ku Rome m’dziko la Italy komwe akuyembekezeka kugwila ntchito za boma ku Vatican komanso mu mzinda wa Rome. Pofika pa...
Kazembe oyimila dziko la Malawi ku Vatican a Joseph Mpinganjira ati kukumana kwa prezidenti Dr Lazarus Chakwera ndi mtsogoleri wa mpingo wa akatolika pa dziko...