Category : Nkhani
Jiya wayamikira chitukuko, wadzudzula mchitidwe oononga
Phungu wadera la pakati munzinda wa Lilongwe wayamika boma kaamba ka ntchito zachitukuko zomwe likugwira mdera lawo. Phunguyi, a Alfred Jiya, wati boma lawamangira misewu...
Mutharika wati aMalawi adzilima mbewu zopilira ng’amba
Mtsogoleri wakale wadziko lino, Professor Peter Mutharika, wapempha anthu m’dziko muno kuti adzitenga mbewu zina ngati chakudya mmalo momangodalira nsima. A Mutharika anena izi pa...
Ulumali si kulephera — Papkid
Oyimba Kennedy ‘Papkid’ Kadewere wati sikoyenera kuti anthu aulumali adzitengedwa ngati olephera m’dziko muno. Iye wapemphanso a Malawi kuti adziyika chidwi pothandizana ndi anthu oterewa...
Ana 169 apulumutsidwa ku maukwati
Dera la mfumu yaikulu Chiseka m’boma la Lilongwe lakwanitsa kuchotsa ana okwana 169 ku mabanja a ana kuyambira mu chaka cha 2023 kufikira pano, adindo...
‘Boma liteteze atsikana nthawi ya ngozi zadzidzidzi’
Bungwe la Green Girls Club lapempha unduna wa za achinyamata kuti uyike njira zoteteza atsikana pa nthawi imene kwagwa ngozi zadzidzidzi, maka zakudza kaamba ka...

