Apolisi kwa Chimwala ku Mangochi akusunga mchitokosi Isaac Mathipa wazaka 35 yemwe ndi mphunzitsi wapasukulu ya sekondale ya Chiunda Community Day pomuganizira kuti wagwilira ophunzira...
Kampani ya zomangamanga ya SICO Holdings yayamikira a New Dawn Boxing Promotion, amene akuti amapereka malipoto abwino akalandira thandizo la ndalama. Mkulu wa kampaniyi, a...
Sukulu ya ukachenjede ya MUST m’boma la Thyolo yakonzeka kuchititsa chionetsero cha chikhalidwe, kafukufuku ndi luso cha chaka chino, kuchokera pa 4 mpaka pa 5...
Ophunzira wa Form 4 pasukulu ya Sharpevalle Community Day Secondary school ku Ntcheu, Tracy Msowoya, wati maphunziro ake tsopano ayenda bwino kutsatira Chipinda chogonamo atsikana...
Apolisi ku Mulanje amanga anthu asanu powaganizira kuti atentha ndi moto khola la ng’ombe komanso nyumba ati pobwezera kuphedwa kwa m’bale wawo, yemwe anthu okwiya...
Timu yadziko lino ya anyamata osapitilira zaka 20 yatuluka mu mpikisano wachaka chino wa COSAFA pamene yagonja masewero otsiriza ndi Lesotho 3-2. Hermas Masinja ndi...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wati zokambirana zomwe bungwe la NEEF likuchita ndi anthu zikuthandiza kuti anthu amvetse ndikutsatira momwe ngongole...
Pamene chipani cha UTM chikukonzekera kudzachita msonkhano wake waukulu mwezi wa mawa, mlembi wamkulu wa chipanichi, a Patricia Kaliati, alengeza kuti adzapikisana nawo pa udindo...
Anthu omwe amasungitsa ndalama zawo mu banki zosiyasiyana m’dziko muno akhala ndi chitsimikizo chochuluka cha chitetezo pa nthawi yomwe bank zingalephere kupitiriza ntchito. Izi zili...