Mtsogoleri wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers, Thom Mpinganjira wapepesa otsatira timu yi chifukwa chogonja ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets dzulo loweluka ndizigoli...
Bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) lati achinyamata sakubweza ngongole za bungweli moyenera akayerekeza ndi magulu ena amene akutenga ngongolezi. Wapampando wa board ya...
Hope Msukwa, amene ndi wa zaka 18, wapambana pa mpikisano okwera njinga zamoto kumapiri aku Misuku m’boma la Chitipa. Iyeyu wapambana atayendetsa njinga yamoto kwa...
Anthu a chikhalidwe cha a Chewa athira nsembe ku Nsinja m’boma la Lilongwe ndipo apempha mphambe kuti akwaniritse zosowa zawo. Kumwambowu, umene unalipo Loweruka, kunali...
Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati sichichita nawo ndale zoononga, zodana komanso zolozana zala ndipo m’malo mwake chipitiriza kugwira ntchito za chitukuko zolozeka zimene zitasinthe...
Katswiri oyimba nyimbo za chamba cha Reggae, Burning Spear, wapereka gitala yake imene wakhala akuyigwiritsa ntchito kwa nthawi yayitali kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr...
Khonsolo ya mnzinda wa Blantyre yakhazikitsa ntchito yomanga zikwangwani zodziwitsa anthu kuti akulowa kapena kutuluka munzindawu. Pokhazikitsa ntchitoyi kwa Kameza, mfumu ya mnzindawu, a Joseph...
Bwalo lalikulu la milandu munzinda wa Blantyre likuyembekezeka kupereka chigamulo lero pa mlandu umene anthu ena anakamang’ala kuti bwaloli liwapatse chiletso kuti bungwe la MEC...
Oyimba nyimbo za uzimu, mayi busa Mary Thuya, ati chimbale chimene akutulutsa chotchedwa “Ndathokoza” ayimba pothokoza Mulungu kaamba kowachiritsa ku matenda a Covid-19. A Thuya...